Ekisodo 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 25:36, 37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Musamalandire chiwongoladzanja kapena kupezerapo phindu+ pa iye.* Muziopa Mulungu wanu+ ndipo mʼbale wanu azikhala ndi moyo pakati panu. 37 Mukamukongoza ndalama musamafunepo chiwongoladzanja+ kapena kumupatsa chakudya kuti mupezerepo phindu. Nehemiya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
36 Musamalandire chiwongoladzanja kapena kupezerapo phindu+ pa iye.* Muziopa Mulungu wanu+ ndipo mʼbale wanu azikhala ndi moyo pakati panu. 37 Mukamukongoza ndalama musamafunepo chiwongoladzanja+ kapena kumupatsa chakudya kuti mupezerepo phindu.