Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 17:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 19:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati munthu wakonzera mnzake chiwembu nʼkupereka umboni wonama wakuti waphwanya lamulo,+ 17 anthu awiri amene akukanganawo aziima pamaso pa Yehova, kapena kuti pamaso pa ansembe ndi oweruza amene akuweruza masiku amenewo.+
16 Ngati munthu wakonzera mnzake chiwembu nʼkupereka umboni wonama wakuti waphwanya lamulo,+ 17 anthu awiri amene akukanganawo aziima pamaso pa Yehova, kapena kuti pamaso pa ansembe ndi oweruza amene akuweruza masiku amenewo.+