-
Rute 4:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Boazi anati: “Ukadzagula malowo kwa Naomi, ndiye kuti wagulanso kwa Rute wa ku Mowabu, amene mwamuna wake anamwalira, kuti dzina la mwamuna wakeyo libwerere pacholowa chake.”+
-