Ekisodo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ koma pano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakumwamba.”+ Salimo 105:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu anachititsa kuti anthu ake aberekane kwambiri,+Iye anawachititsa kuti akhale amphamvu kwambiri kuposa adani awo.+
22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ koma pano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakumwamba.”+
24 Mulungu anachititsa kuti anthu ake aberekane kwambiri,+Iye anawachititsa kuti akhale amphamvu kwambiri kuposa adani awo.+