Ekisodo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibe munthu amene adzalimbane nanu.+ Yehova Mulungu wanu adzachititsa dziko lonse limene mudzayendemo kugwidwa ndi mantha aakulu ndipo adzakuopani,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani. Yoswa 2:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
25 Palibe munthu amene adzalimbane nanu.+ Yehova Mulungu wanu adzachititsa dziko lonse limene mudzayendemo kugwidwa ndi mantha aakulu ndipo adzakuopani,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.