-
Numeri 21:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi nʼkuyamba kukhala mʼmizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni ndi mʼmidzi yake yonse yozungulira.
-