-
1 Samueli 4:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Komanso Likasa la Mulungu linalandidwa, ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana a Eli, anaphedwa.+
-
-
1 Samueli 5:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Afilisiti atalanda Likasa+ la Mulungu woona, analitenga ku Ebenezeri nʼkupita nalo ku Asidodi.
-
-
Salimo 78:61Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
61 Analola kuti adani atenge chizindikiro cha mphamvu zake,
Analola kuti ulemerero wake ukhale mʼmanja mwa adani.+
-