Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 31:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Afilisiti anayamba kumenyana ndi Aisiraeli+ ndipo asilikali a Isiraeli ankathawa moti ambiri anaphedwa mʼphiri la Giliboa.+

  • 1 Samueli 31:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho Sauli, ana ake atatu, womunyamulira zida komanso asilikali ake onse anafera limodzi pa tsikuli.+

  • 1 Mbiri 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako Sauli anauza womunyamulira zida kuti: “Solola lupanga lako undibaye kuti anthu osadulidwawa asandipeze nʼkundipha mwankhanza.”+ Koma womunyamulira zidayo sankafuna chifukwa ankachita mantha kwambiri. Choncho Sauli anatenga lupanga lake nʼkuligwera.+

  • 1 Mbiri 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho Sauli ndi ana ake atatu anafa ndipo anthu onse amʼnyumba yake anafera limodzi.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani