-
1 Mbiri 10:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Afilisiti anayamba kumenyana ndi Aisiraeli ndipo asilikali a Isiraeli ankathawa moti ambiri anaphedwa mʼphiri la Giliboa.+
-