-
1 Samueli 31:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Nkhondo inamʼkulira kwambiri Sauli, moti oponya mivi ndi uta anamupeza nʼkumuvulaza koopsa.+
-
-
1 Mbiri 10:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Nkhondo inamukulira kwambiri Sauli, moti kenako oponya mivi ndi uta anamupeza nʼkumuvulaza.+
-