Levitiko 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzawononga malo anu opatulika olambirirako+ ndipo ndidzagwetsa maguwa anu ofukizirapo zonunkhira. Ndidzaunjika mitembo yanu pamwamba pa mafano anu onyansa* opanda moyowo,+ ndipo ndidzachoka pakati panu monyansidwa.+ Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
30 Ndidzawononga malo anu opatulika olambirirako+ ndipo ndidzagwetsa maguwa anu ofukizirapo zonunkhira. Ndidzaunjika mitembo yanu pamwamba pa mafano anu onyansa* opanda moyowo,+ ndipo ndidzachoka pakati panu monyansidwa.+