-
Amosi 5:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Chifukwa ndikudziwa kuchuluka kwa zochita zanu zondigalukira,
Ndiponso kukula kwa machimo anu.
Mumachitira nkhanza munthu wolungama,
Mumalandira ziphuphu,
Komanso mumaphwanya ufulu wa anthu osauka pageti la mzinda.+
-
-
Habakuku 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho lamulo latha mphamvu,
Ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.
Oipa akupondereza anthu olungama,
Nʼchifukwa chake chilungamo chikupotozedwa.+
-