-
1 Mafumu 4:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Solomo anali ndi nduna 12 zomwe zinkayangʼanira Aisiraeli onse ndipo zinkabweretsa chakudya kwa mfumu ndi banja lake. Nduna iliyonse inkabweretsa chakudya kwa mwezi umodzi pachaka.+
-