-
Ezekieli 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 ‘Koma ngati mneneri wapusitsidwa nʼkupereka yankho, ineyo Yehova ndi amene ndapusitsa mneneriyo.+ Choncho ndidzatambasula dzanja langa nʼkumuwononga kuti asakhalenso pakati pa anthu anga, Aisiraeli.
-