-
2 Mbiri 20:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Yehosafati anapitiriza kulamulira ku Yuda. Iye anali ndi zaka 35 pamene ankakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba mwana wa Sili.+
-