-
2 Mbiri 21:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako Yehosafati, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide. Ndiyeno mwana wake Yehoramu anakhala mfumu mʼmalo mwake.+
-
-
2 Mbiri 21:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Yehoramu anakhala mfumu ali ndi zaka 32 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8.+
-