-
1 Mafumu 16:31, 32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ngati kuti kuyenda mʼmachimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati kunali kosakwanira, Ahabu anakwatira Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kutumikira Baala+ nʼkumamugwadira. 32 Kuwonjezera pamenepo, anamanga guwa lansembe la Baala mʼkachisi wa Baala+ amene iye anamanga ku Samariya.
-