-
2 Mafumu 23:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Komabe Yehova sanabweze mkwiyo wake waukulu umene anakwiyira Yuda, chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene Manase anachita nʼkumukwiyitsa.+
-