-
1 Mbiri 29:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Yehova anakweza kwambiri Solomo pamaso pa Aisiraeli onse nʼkumupatsa ulemu waukulu wachifumu kuposa mfumu ina iliyonse imene inalamulira Isiraeli iye asanakhale mfumu.+
-
-
Mlaliki 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo ndinapitiriza kuchitabe zinthu mwanzeru.
-