-
1 Mbiri 21:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga mʼchipululu ndiponso guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibiyoni.+
-