-
1 Mbiri 28:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzamange nyumba yanga ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndamusankha kuti akhale mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+
-
-
Salimo 132:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yehova walumbira kwa Davide.
Ndithudi sadzalephera kukwaniritsa mawu ake akuti:
-