2 Mafumu 21:7-9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova anati: “Yuda nayenso ndidzamʼchotsa pamaso panga+ ngati mmene ndinachotsera Isiraeli+ ndipo ndidzakana mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala kumeneko.’”+ 2 Mbiri 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
27 Yehova anati: “Yuda nayenso ndidzamʼchotsa pamaso panga+ ngati mmene ndinachotsera Isiraeli+ ndipo ndidzakana mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala kumeneko.’”+