Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yoswa 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo ndinakufikitsani kudziko la Aamori amene ankakhala kutsidya lina* la Yorodano. Iwo anayamba kumenyana nanu+ koma ndinawapereka mʼmanja mwanu kuti mutenge dziko lawo kukhala lanu moti ndinawafafaniza pamaso panu.+

  • 2 Mafumu 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Manase mfumu ya Yuda wachita zinthu zonyansa zonsezi. Wachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu.+ Iye wachititsa Yuda kuchimwa ndi mafano ake onyansa.*

  • 2 Mafumu 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Manase anaphanso anthu ambiri osalakwa mpaka magazi awo anadzaza Yerusalemu kuyambira koyambirira mpaka kumapeto,+ kuwonjezera pa tchimo lake lochititsa kuti Ayuda achimwe pochita zoipa pamaso pa Yehova.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani