2 Mbiri 33:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+ 2 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova ndipo ankatsatira zinthu zonyansa zomwe ankachita anthu a mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa Aisiraeli.+
33 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+ 2 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova ndipo ankatsatira zinthu zonyansa zomwe ankachita anthu a mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa Aisiraeli.+