-
2 Mbiri 25:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Amaziya atasiya kutsatira Yehova, anthu anamʼkonzera chiwembu+ ku Yerusalemu ndipo iye anathawira ku Lakisi. Koma anthuwo anatumiza anthu ena omwe anamutsatira ku Lakisiko nʼkukamuphera komweko.
-