2 Mafumu 21:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhani zina zokhudza Amoni ndiponso zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda. 26 Choncho anamuika mʼmanda ake mʼmunda wa Uziza+ ndipo mwana wake Yosiya+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
25 Nkhani zina zokhudza Amoni ndiponso zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda. 26 Choncho anamuika mʼmanda ake mʼmunda wa Uziza+ ndipo mwana wake Yosiya+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.