1 Mbiri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya+ ndipo wa 4 anali Salumu. Yeremiya 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ponena za Salumu*+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, amene akulamulira mʼmalo mwa bambo ake Yosiya,+ amene anachoka mʼdziko lino kupita ku ukapolo, Yehova wanena kuti: ‘Sadzabwereranso kwawo.
15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya+ ndipo wa 4 anali Salumu.
11 Ponena za Salumu*+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, amene akulamulira mʼmalo mwa bambo ake Yosiya,+ amene anachoka mʼdziko lino kupita ku ukapolo, Yehova wanena kuti: ‘Sadzabwereranso kwawo.