Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yoswa 19:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Me-jarikoni ndi Rakoni, nʼkukafika kumalire amene ali kutsogolo kwa Yopa.+

  • Yoswa 19:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ichi chinali cholowa cha fuko la Dani motsatira mabanja awo, ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.

  • Ezara 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako anthuwo anapereka ndalama kwa anthu osema miyala+ ndi amisiri.+ Anaperekanso chakudya, zakumwa ndi mafuta kwa anthu a ku Sidoni ndi ku Turo chifukwa anabweretsa matabwa a mkungudza kudzera panyanja kuchokera ku Lebanoni kukafika ku Yopa.+ Anachita zimenezi mogwirizana ndi chilolezo chimene Koresi mfumu ya ku Perisiya anawapatsa.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani