-
Ezara 7:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Zinthu zina zonse zofunika panyumba ya Mulungu wako zimene ukuyenera kupereka, ukazitenge kunyumba yosungiramo chuma cha mfumu.+
-
-
Yesaya 49:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mafumu adzakhala okusamalira,+
Ndipo ana awo aakazi adzakhala okuyamwitsira ana ako.
-