Ezara 5:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zekariya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mʼmwezi wa 8, mʼchaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya*+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido, kuti: Zekariya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku la 24 la mwezi wa 11 womwe ndi mwezi wa Sebati,* mʼchaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido. Anamuuza kuti anene kuti: Zekariya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Mʼmwezi wa 8, mʼchaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya*+ mwana wa Berekiya, mwana wa Ido, kuti:
7 Pa tsiku la 24 la mwezi wa 11 womwe ndi mwezi wa Sebati,* mʼchaka chachiwiri cha ulamuliro wa Dariyo,+ Yehova analankhula ndi mneneri Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido. Anamuuza kuti anene kuti: