-
Ezara 6:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mulungu amene anaika dzina lake kumeneko,+ achotse mfumu iliyonse ndi anthu alionse ophwanya lamulo limeneli ndiponso owononga nyumba ya Mulungu imene ili ku Yerusalemu. Ine Dariyo ndaika lamulo limeneli, ndipo zichitike mwamsanga.”
-