1 Mbiri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+ Nehemiya 7:73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Ndiyeno ansembe, Alevi, alonda apageti, oimba,+ anthu ena, atumiki apakachisi* ndiponso Aisiraeli onse anayamba kukhala mʼmizinda yawo.+ Pofika mwezi wa 7,+ Aisiraeli anali atakhala mʼmizinda yawo.+
2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+
73 Ndiyeno ansembe, Alevi, alonda apageti, oimba,+ anthu ena, atumiki apakachisi* ndiponso Aisiraeli onse anayamba kukhala mʼmizinda yawo.+ Pofika mwezi wa 7,+ Aisiraeli anali atakhala mʼmizinda yawo.+