Ezara 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena mwa Aisiraeli, ansembe, Alevi,+ oimba,+ alonda apageti+ ndi atumiki apakachisi*+ anapita ku Yerusalemu mʼchaka cha 7 cha mfumu Aritasasita.
7 Ena mwa Aisiraeli, ansembe, Alevi,+ oimba,+ alonda apageti+ ndi atumiki apakachisi*+ anapita ku Yerusalemu mʼchaka cha 7 cha mfumu Aritasasita.