2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Ezara 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ezara anabwera kuchokera ku Babulo. Iye anali wokopera* Malemba ndipo ankadziwa bwino* Chilamulo cha Mose+ chimene Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka. Mfumu inamupatsa zonse zimene anapempha chifukwa dzanja la Yehova Mulungu wake linkamuthandiza. Ezara 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
6 Ezara anabwera kuchokera ku Babulo. Iye anali wokopera* Malemba ndipo ankadziwa bwino* Chilamulo cha Mose+ chimene Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka. Mfumu inamupatsa zonse zimene anapempha chifukwa dzanja la Yehova Mulungu wake linkamuthandiza.