-
Ezara 8:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndinawasonkhanitsa pamtsinje umene umafika ku Ahava+ ndipo tinamanga msasa pamenepo nʼkukhalapo masiku atatu. Koma nditafufuza bwinobwino anthuwo komanso ansembe, sindinapezepo Alevi.
-