Nehemiya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ansembe ndi Alevi amene anapita ndi Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi Yesuwa+ ndi awa: Seraya, Yeremiya, Ezara, Nehemiya 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno panali Alevi awa: Yesuwa, Binui, Kadimiyeli,+ Serebiya, Yuda ndiponso Mataniya,+ amene ankatsogolera nyimbo zotamanda Mulungu limodzi ndi abale ake.
12 Ansembe ndi Alevi amene anapita ndi Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi Yesuwa+ ndi awa: Seraya, Yeremiya, Ezara,
8 Ndiyeno panali Alevi awa: Yesuwa, Binui, Kadimiyeli,+ Serebiya, Yuda ndiponso Mataniya,+ amene ankatsogolera nyimbo zotamanda Mulungu limodzi ndi abale ake.