Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba imene ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Aisiraeli adzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+

  • Nehemiya 9:36, 37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Pano ndife akapolo.+ Ndife akapolo mʼdziko limene munapatsa makolo athu kuti adye zipatso zake ndi zinthu zake zabwino. 37 Mafumu amene mwalola kuti azitilamulira chifukwa cha machimo athu+ ndi amene akusangalala ndi zokolola zochuluka zamʼdzikoli. Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.

  • Salimo 79:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani