Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Esitere 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno inu mfumu musankhe anthu mʼzigawo zonse za ufumu wanu.+ Anthuwo asonkhanitse anamwali okongola kunyumba ya mfumu ya ku Susani* yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ndipo azikhala mʼnyumba ya akazi. Atsikanawa aziyangʼaniridwa ndi Hegai,+ munthu wofulidwa wa mfumu amene amayangʼanira akazi. Ndipo kumeneko atsikanawo azikawapaka mafuta okongoletsa.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani