Esitere 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando akalonga ndi atumiki ake onse. Asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka ndiponso akalonga amʼzigawo za ufumu wake analinso pomwepo.
3 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando akalonga ndi atumiki ake onse. Asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka ndiponso akalonga amʼzigawo za ufumu wake analinso pomwepo.