-
Salimo 119:73Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
73 Manja anu anandipanga komanso kundiumba.
Ndithandizeni kuti ndikhale wozindikira,
Kuti ndiphunzire malamulo anu.+
-