-
Yesaya 38:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndadzitonthoza mpaka mʼmawa.
Mofanana ndi mkango, iye akungokhalira kuphwanya mafupa anga onse.
Kuyambira mʼmawa mpaka usiku mukuchititsa kuti ndithe pangʼonopangʼono.+
-