Yobu 8:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimenezi ndi zimene zidzachitikire* anthu onse amene aiwala Mulungu,Chifukwa chiyembekezo cha anthu oipa* chidzatha.14 Amene amadalira zinthu zosathandiza,Amene amadalira zinthu zosalimba ngati ulusi wa kangaude.* Yobu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yobu 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye adzachotsedwa mʼmalo otetezeka amutenti yake,+Ndipo adzamupititsa kwa mfumu ya zinthu zoopsa.*
13 Zimenezi ndi zimene zidzachitikire* anthu onse amene aiwala Mulungu,Chifukwa chiyembekezo cha anthu oipa* chidzatha.14 Amene amadalira zinthu zosathandiza,Amene amadalira zinthu zosalimba ngati ulusi wa kangaude.*
14 Iye adzachotsedwa mʼmalo otetezeka amutenti yake,+Ndipo adzamupititsa kwa mfumu ya zinthu zoopsa.*