-
2 Mafumu 6:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Mfumuyo itangomva mawu a mayiyo, inangʼamba zovala zake.+ Pamene inkayenda pamwamba pa khomalo, anthu anaona kuti yavala chiguduli mkati.
-