-
Maliro 1:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndikulira chifukwa cha zinthu zimenezi.+ Misozi ikutuluka mʼmaso mwanga.
Chifukwa aliyense amene akananditonthoza kapena kunditsitsimula, ali kutali ndi ine.
Ana anga awonongedwa ndipo mdani wanga wapambana.
-