-
Salimo 72:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Adzawapulumutsa* kuti asaponderezedwe komanso kuchitiridwa zachiwawa,
Ndipo adzaona kuti magazi awo ndi amtengo wapatali.
-