Yobu 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zikanakhala bwino wina akanandimvetsera.+ Ndikanasainira dzina langa pa zimene ndanena.* Wamphamvuyonse andiyankhe.+ Zikanakhala bwino munthu amene akundiimba mlandu akanalemba milandu yanga papepala.
35 Zikanakhala bwino wina akanandimvetsera.+ Ndikanasainira dzina langa pa zimene ndanena.* Wamphamvuyonse andiyankhe.+ Zikanakhala bwino munthu amene akundiimba mlandu akanalemba milandu yanga papepala.