-
Yobu 8:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Zimenezi ndi zimene zidzachitikire* anthu onse amene aiwala Mulungu,
Chifukwa chiyembekezo cha anthu oipa* chidzatha.
-
Yobu 21:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Chifukwa mukunena kuti, ‘Kodi nyumba ya munthu wolemekezeka ili kuti,
Nanga tenti imene munthu woipa ankakhala ili kuti?’+
-
-
-