-
Yobu 15:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Amamva phokoso lochititsa mantha mʼmakutu ake,+
Pa nthawi yamtendere achifwamba amamuukira.
-
-
Yobu 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Zoopsa zimamuchititsa mantha paliponse,+
Ndipo zimamuthamangitsa zili naye pafupi kwambiri.
-