-
Yobu 31:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ngati ndinkasangalala chifukwa chakuti ndinali ndi chuma chochuluka,+
Chifukwa cha zinthu zambiri zimene ndinapeza,+
-
Yobu 31:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Chimenecho chikanakhala cholakwa chimene oweruza akuyenera kundipatsa chilango,
Chifukwa ndikanakhala nditakana Mulungu woona wakumwamba.
-
-
-