-
Yobu 10:18, 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiye nʼchifukwa chiyani munanditulutsa mʼmimba mwa mayi anga?+
Zikanakhala bwino ndikanafa diso lililonse lisanandione.
19 Zikanakhala ngati sindinakhaleko.
Ndikanangochokera mʼmimba nʼkupita kumanda.’
-